Amosi 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamvani izi, inu amene mumapondaponda anthu osauka,Ndiponso amene mumapha anthu ofatsa mʼdzikoli.+