-
Amosi 8:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthu adzayenda modzandira kuchokera kunyanja mpaka kukafika kunyanja,
Kuchokera kumpoto mpaka kukafika kumʼmawa.
Iwo adzayenda uku ndi uku pofunafuna mawu a Yehova, koma sadzawapeza.
-