Amosi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akadzatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo,Kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+Ndidzakhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka, osati kuwapatsa madalitso.+
4 Akadzatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo,Kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+Ndidzakhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka, osati kuwapatsa madalitso.+