Amosi 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika,Pamene wolima adzapitirira wokolola,Ndipo woponda mphesa adzapitirira wonyamula mbewu.+Mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera+Ndipo mʼmapiri angʼonoangʼono muzidzatuluka vinyo wambiri.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:13 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 18
13 Yehova wanena kuti, ‘Masiku adzafika,Pamene wolima adzapitirira wokolola,Ndipo woponda mphesa adzapitirira wonyamula mbewu.+Mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera+Ndipo mʼmapiri angʼonoangʼono muzidzatuluka vinyo wambiri.+