-
Yona 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako Yona analowa mumzindawo nʼkuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Iye ankalalikira kuti: “Kwangotsala masiku 40 okha ndipo Nineve awonongedwa.”
-