Yona 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Yona anatuluka mumzindawo nʼkukakhala pansi kumʼmawa kwa mzindawo. Kumeneko anamanga kachisakasa kuti akhale pamthunzi podikira kuti aone zimene zichitikire mzindawo.+
5 Kenako Yona anatuluka mumzindawo nʼkukakhala pansi kumʼmawa kwa mzindawo. Kumeneko anamanga kachisakasa kuti akhale pamthunzi podikira kuti aone zimene zichitikire mzindawo.+