Yona 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova Mulungu anameretsa chomera cha mtundu wa mphonda* kuti chiyange pamene Yona anakhala. Anachita zimenezi kuti pakhale mthunzi nʼcholinga choti apeze mpumulo. Yona anasangalala kwambiri chifukwa cha chomeracho.
6 Ndiyeno Yehova Mulungu anameretsa chomera cha mtundu wa mphonda* kuti chiyange pamene Yona anakhala. Anachita zimenezi kuti pakhale mthunzi nʼcholinga choti apeze mpumulo. Yona anasangalala kwambiri chifukwa cha chomeracho.