Yona 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Mulungu anafunsa Yona kuti: “Kodi pali chifukwa choti ukwiyire ndi chomera cha mtundu wa mphondachi?”+ Yona anayankha kuti: “Ndikuyeneradi kukwiya, ndakwiya kwambiri moti ndikufuna kufa.” Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,9/15/1986, ptsa. 28-29
9 Ndiyeno Mulungu anafunsa Yona kuti: “Kodi pali chifukwa choti ukwiyire ndi chomera cha mtundu wa mphondachi?”+ Yona anayankha kuti: “Ndikuyeneradi kukwiya, ndakwiya kwambiri moti ndikufuna kufa.”