-
Habakuku 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Nʼchifukwa chiyani mukuchititsa munthu kukhala ngati nsomba zamʼnyanja,
Ndiponso ngati zokwawa zimene zilibe mtsogoleri?
-