Habakuku 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinaona mahema a Kusani ali ndi nkhawa. Nsalu za mahema za ku Midiyani zinanjenjemera.+