Habakuku 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nditamva mawu ake, mʼmimba mwanga munabwadamuka.Ndipo milomo yanga inanjenjemera. Mafupa anga anayamba kuwola,+Ndipo miyendo yanga inanjenjemera. Koma ndikuyembekezera mofatsa tsiku la masautso.+Chifukwa likubwera kwa anthu amene amatiukira. Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, tsa. 17 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, ptsa. 23-24
16 Nditamva mawu ake, mʼmimba mwanga munabwadamuka.Ndipo milomo yanga inanjenjemera. Mafupa anga anayamba kuwola,+Ndipo miyendo yanga inanjenjemera. Koma ndikuyembekezera mofatsa tsiku la masautso.+Chifukwa likubwera kwa anthu amene amatiukira.