-
Hagai 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 “Ngati munthu atanyamula nyama yopatulika pachovala chake, ndiyeno chovalacho nʼkukhudza mkate, kapena msuzi, kapena vinyo, kapena mafuta, kapena chakudya chilichonse, kodi chinthu chokhudzidwacho chingakhale chopatulika?”’”
Ansembewo anayankha kuti: “Ayi!”
-