-
Hagai 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho Hagai anati: “‘Mmenemutu ndi mmene anthu awa alili ndipo ndi mmene mtunduwu ulili pamaso panga. Ndi mmenenso ntchito yonse ya manja awo ndi chilichonse chimene amapereka nsembe chilili. Ndi zodetsedwa,’ watero Yehova.
-