Hagai 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Koma tsopano, chonde ganizirani izi mofatsa kuyambira lero mpaka mʼtsogolo: Asanasanjikize mwala pamwala unzake mʼkachisi wa Yehova,+ Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Nsanja ya Olonda,1/1/1997, ptsa. 17-22
15 ‘Koma tsopano, chonde ganizirani izi mofatsa kuyambira lero mpaka mʼtsogolo: Asanasanjikize mwala pamwala unzake mʼkachisi wa Yehova,+