Hagai 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Lero, pa tsiku la 24 la mwezi wa 9, pamene maziko a kachisi wa Yehova ayalidwa,+ kuyambira lero kupita mʼtsogolo, chonde ganizirani izi mofatsa: Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Nsanja ya Olonda,1/1/1997, ptsa. 17-22
18 ‘Lero, pa tsiku la 24 la mwezi wa 9, pamene maziko a kachisi wa Yehova ayalidwa,+ kuyambira lero kupita mʼtsogolo, chonde ganizirani izi mofatsa: