Hagai 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi mbewu zilipobe mʼnyumba yosungiramo mbewu?*+ Kodi mitengo ya mpesa, ya mkuyu, ya makangaza* ndi ya maolivi yabereka zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+ Hagai Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, ptsa. 26-27
19 Kodi mbewu zilipobe mʼnyumba yosungiramo mbewu?*+ Kodi mitengo ya mpesa, ya mkuyu, ya makangaza* ndi ya maolivi yabereka zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+