Zekariya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Bwererani kwa ine,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, “ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.’” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 31
3 Uwauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Bwererani kwa ine,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, “ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.’”