Zekariya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndinaona masomphenya usiku. Ndinaona munthu atakwera pahatchi* yomwe inaima pakati pa mitengo ya mchisu imene inali mʼchigwa. Kumbuyo kwake kunali mahatchi ofiira kwambiri, ofiirira ndi oyera.”*
8 “Ndinaona masomphenya usiku. Ndinaona munthu atakwera pahatchi* yomwe inaima pakati pa mitengo ya mchisu imene inali mʼchigwa. Kumbuyo kwake kunali mahatchi ofiira kwambiri, ofiirira ndi oyera.”*