-
Zekariya 1:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Choncho ndinafunsa kuti: “Kodi amenewa ndi ndani mbuyanga?”
Mngelo amene ankalankhula nane anandiyankha kuti: “Ndikuuza kuti amenewa ndi ndani.”
-