Zekariya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho ndinafunsa mngelo amene ankalankhula nane uja kuti: “Kodi nyangazi zikuimira chiyani?” Iye anandiyankha kuti: “Izi ndi nyanga zimene zinabalalitsa Yuda,+ Isiraeli+ ndi Yerusalemu.”+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 30
19 Choncho ndinafunsa mngelo amene ankalankhula nane uja kuti: “Kodi nyangazi zikuimira chiyani?” Iye anandiyankha kuti: “Izi ndi nyanga zimene zinabalalitsa Yuda,+ Isiraeli+ ndi Yerusalemu.”+