Zekariya 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mngeloyo anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona mpukutu ukuuluka. Mpukutuwo ndi wautali mikono* 20 mulitali ndiponso mikono 10 mulifupi.” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 22
2 Mngeloyo anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona mpukutu ukuuluka. Mpukutuwo ndi wautali mikono* 20 mulitali ndiponso mikono 10 mulifupi.”