-
Zekariya 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mngelo uja anandiuza kuti: “Mayi ameneyu dzina lake ndi Kuipa.” Kenako anamukankha nʼkumubwezera mʼchiwiya chokwana muyezo wa efacho ndipo anachivundikira ndi chivundikiro chamtovu chija.
-