Zekariya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Galeta loyamba linkakokedwa ndi mahatchi ofiira ndipo galeta lachiwiri linkakokedwa ndi mahatchi akuda.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 27
2 Galeta loyamba linkakokedwa ndi mahatchi ofiira ndipo galeta lachiwiri linkakokedwa ndi mahatchi akuda.+