Zekariya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Galeta lachitatu linkakokedwa ndi mahatchi oyera ndipo galeta la 4 linkakokedwa ndi mahatchi amawangamawanga ndiponso amadonthomadontho.+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 27
3 Galeta lachitatu linkakokedwa ndi mahatchi oyera ndipo galeta la 4 linkakokedwa ndi mahatchi amawangamawanga ndiponso amadonthomadontho.+