-
Zekariya 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mahatchi amadonthomadontho anali okonzeka kupita nʼkumakayendayenda padziko lapansi.” Kenako iye anauza mahatchiwo kuti: “Pitani mukayendeyende padziko lapansi.” Ndipo mahatchiwo anapita nʼkumakayendayenda padziko lapansi.
-