-
Zekariya 6:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mngelo uja anandiitana nʼkundiuza kuti: “Taona, mkwiyo umene Yehova anali nawo padziko lakumpoto watha chifukwa cha mahatchi amene apita kumeneko.”
-