-
Zekariya 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 “Ukatenge kwa Heledai, Tobiya ndi Yedaya zinthu zimene abweretsa kuchokera kwa anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo. Pa tsiku limenelo udzapite kunyumba ya Yosiya mwana wa Zefaniya pamodzi ndi anthu amene achokera ku Babulowo.
-