Zekariya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chisoti chachifumucho* chizidzakhala mʼkachisi wa Yehova kuti anthu azidzakumbukira Helemu, Tobiya, Yedaya+ ndi Heni mwana wa Zefaniya. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 30
14 Chisoti chachifumucho* chizidzakhala mʼkachisi wa Yehova kuti anthu azidzakumbukira Helemu, Tobiya, Yedaya+ ndi Heni mwana wa Zefaniya.