Zekariya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi imeneyi isanafike, palibe malipiro omwe ankaperekedwa polipira munthu kapena chiweto.+ Zinali zoopsa kuyenda ulendo chifukwa cha adani, popeza ine ndinkachititsa kuti anthu onse aziukirana.’ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 19
10 Nthawi imeneyi isanafike, palibe malipiro omwe ankaperekedwa polipira munthu kapena chiweto.+ Zinali zoopsa kuyenda ulendo chifukwa cha adani, popeza ine ndinkachititsa kuti anthu onse aziukirana.’