-
Zekariya 10:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ngakhale kuti ndidzawamwaza ngati mbewu pakati pa anthu a mitundu ina,
Iwo adzandikumbukira ali kumadera akutali.
Iwowo ndi ana awo adzapezanso mphamvu ndipo adzabwerera.
-