Zekariya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Mafumu a Yuda adzanena mumtima mwawo kuti, ‘Anthu a ku Yerusalemu akutipatsa mphamvu chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi Mulungu wawo.’+ Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Nsanja ya Olonda,12/15/2007, ptsa. 24-256/15/1989, ptsa. 30-31
5 “Mafumu a Yuda adzanena mumtima mwawo kuti, ‘Anthu a ku Yerusalemu akutipatsa mphamvu chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi Mulungu wawo.’+