Zekariya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Lidzakhala tsiku limodzi lotchedwa tsiku la Yehova.+ Sikudzakhala masana kapena usiku, chifukwa ngakhale usiku kudzakhala kukuwalabe. Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:7 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, tsa. 29
7 Lidzakhala tsiku limodzi lotchedwa tsiku la Yehova.+ Sikudzakhala masana kapena usiku, chifukwa ngakhale usiku kudzakhala kukuwalabe.