Mateyu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamadzinamize kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Chifukwa ndikukuuzani kuti Mulungu akhoza kupangira Abulahamu ana kuchokera kumiyala iyi. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 12
9 Musamadzinamize kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Chifukwa ndikukuuzani kuti Mulungu akhoza kupangira Abulahamu ana kuchokera kumiyala iyi.