-
Mateyu 3:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma Yohane anayesa kumuletsa ponena kuti: “Ineyo ndi amene ndikuyenera kubatizidwa ndi inu, ndiye nʼchifukwa chiyani mukubwera kwa ine?”
-