-
Mateyu 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yesu anamuyankha kuti: “Pa nthawi ino yokha lola kuti zikhale choncho, chifukwa tikufunikira kuchita zimenezi kuti tikwaniritse chilungamo chonse.” Atatero, anasiya kumuletsa.
-