Mateyu 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Uzithetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wakukhoti kuti akuponye mʼndende.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:25 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, ptsa. 6-7
25 Uzithetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wakukhoti kuti akuponye mʼndende.+