Mateyu 5:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake anthu abwino ndi oipa omwe, ndipo amagwetsera mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:45 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, ptsa. 17-18 Yandikirani, ptsa. 272-274 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2016, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,1/1/2009, tsa. 145/15/2008, tsa. 812/1/1989, tsa. 5
45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake anthu abwino ndi oipa omwe, ndipo amagwetsera mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+
5:45 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, ptsa. 17-18 Yandikirani, ptsa. 272-274 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2016, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,1/1/2009, tsa. 145/15/2008, tsa. 812/1/1989, tsa. 5