-
Mateyu 8:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma chakumadzulo, anthu anamubweretsera anthu ambiri ogwidwa ndi ziwanda. Iye anatulutsa mizimu imeneyo ndi mawu okha ndipo anachiritsa anthu onse amene ankadwala.
-