Mateyu 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anachita zimenezi kuti zimene Mulungu ananena kudzera mwa mneneri Yesaya zikwaniritsidwe. Iye ananena kuti: “Iye anatenga matenda athu nʼkunyamula zowawa zathu.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:17 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 11
17 Anachita zimenezi kuti zimene Mulungu ananena kudzera mwa mneneri Yesaya zikwaniritsidwe. Iye ananena kuti: “Iye anatenga matenda athu nʼkunyamula zowawa zathu.”+