-
Mateyu 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Gulu la anthulo litaona zimenezi, linagwidwa ndi mantha ndipo linatamanda Mulungu, amene anapereka mphamvu zimenezo kwa anthu.
-