Mateyu 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atachoka pamenepo, Yesu anaona munthu wina dzina lake Mateyu atakhala mu ofesi yokhomeramo msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Nthawi yomweyo ananyamuka nʼkumutsatira.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,10/15/1987, tsa. 225/15/1986, tsa. 8
9 Atachoka pamenepo, Yesu anaona munthu wina dzina lake Mateyu atakhala mu ofesi yokhomeramo msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Nthawi yomweyo ananyamuka nʼkumutsatira.+