Mateyu 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati samva chisoni ngati mkwatiyo+ ali nawo limodzi, si choncho kodi? Koma masiku akubwera pamene mkwatiyo adzachotsedwa pakati pawo+ ndipo pa nthawiyo adzasala kudya. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 256/1/1986, tsa. 9
15 Yesu anawayankha kuti: “Anzake a mkwati samva chisoni ngati mkwatiyo+ ali nawo limodzi, si choncho kodi? Koma masiku akubwera pamene mkwatiyo adzachotsedwa pakati pawo+ ndipo pa nthawiyo adzasala kudya.