Mateyu 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe amene amasokerera chigamba cha nsalu yatsopano pamalaya akunja akale. Chifukwa chigambacho chingakoke nʼkungʼamba malayawo ndipo kungʼambikako kungawonjezeke kwambiri.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Galamukani!,2/8/1993, tsa. 31 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 256/1/1986, tsa. 9
16 Palibe amene amasokerera chigamba cha nsalu yatsopano pamalaya akunja akale. Chifukwa chigambacho chingakoke nʼkungʼamba malayawo ndipo kungʼambikako kungawonjezeke kwambiri.+
9:16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Galamukani!,2/8/1993, tsa. 31 Nsanja ya Olonda,7/15/1989, tsa. 256/1/1986, tsa. 9