-
Mateyu 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiponso anthu sathira vinyo watsopano mʼmatumba achikopa akale. Akachita zimenezo, matumba achikopawo amaphulika ndipo vinyoyo amatayika moti matumbawo amawonongeka. Koma anthu amathira vinyo watsopano mʼmatumba achikopa atsopano, ndipo zonse ziwiri zimasungika bwino.”
-