Mateyu 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako anawagwira mʼmaso+ nʼkunena kuti: “Mogwirizana ndi chikhulupiriro chanu zimene mukufunazo zichitike kwa inu.”
29 Kenako anawagwira mʼmaso+ nʼkunena kuti: “Mogwirizana ndi chikhulupiriro chanu zimene mukufunazo zichitike kwa inu.”