Mateyu 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiponso aliyense amene sakufuna kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira ndi wosayenera kuti akhale wophunzira wanga.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:38 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2022, tsa. 31
38 Ndiponso aliyense amene sakufuna kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira ndi wosayenera kuti akhale wophunzira wanga.+