-
Mateyu 13:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kenako atauza gulu la anthulo kuti lizipita, analowa mʼnyumba. Ndipo ophunzira ake anabwera kwa iye nʼkunena kuti: “Timasulireni fanizo lija la namsongole mʼmunda.”
-