-
Mateyu 15:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma iye sanamuyankhe chilichonse. Choncho ophunzira ake anabwera nʼkumuuza kuti: “Muuzeni kuti azipita, chifukwa akupitirizabe kufuula mʼmbuyo mwathumu.”
-