Mateyu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anthu ochuluka anabwera kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, a vuto losaona, a vuto losalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana. Anthuwo anawakhazika pamapazi ake ndipo iye anawachiritsa.+
30 Kenako anthu ochuluka anabwera kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, a vuto losaona, a vuto losalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana. Anthuwo anawakhazika pamapazi ake ndipo iye anawachiritsa.+