Mateyu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mfundo yake simukuimvetsabe? Kapena kodi simukukumbukira anthu 5,000 amene anadya mitanda 5 ya mikate, komanso kuchuluka kwa madengu amene munatolera a chakudya chimene chinatsala?+
9 Kodi mfundo yake simukuimvetsabe? Kapena kodi simukukumbukira anthu 5,000 amene anadya mitanda 5 ya mikate, komanso kuchuluka kwa madengu amene munatolera a chakudya chimene chinatsala?+